Genesis 36:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Reuele ndi aŵa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Ameneŵa ndiwo ana a Basemati mkazi wa Esau.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Reuwele: Nahati, ndi Zera, Sama, ndi Miza; amenewa ndi ana a Basemati mkazi wake wa Esau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi ana a Reueli: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Amenewa ndi ana a Basemati, mkazi wa Esau.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Reueli: Nahati, ndi Zera, Sama, ndi Miza; amenewa ndi ana a Basemati mkazi wace wa Esau.