Genesis 36:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Oholibama mkazi wa Esau ndi aŵa: Yeusi, Yalamu ndi Kora. Oholibamayo anali mwana wa Ana mwana wa Zibiyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni, mkazi wake wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Yeusi, ndi Yalamu, ndi Kora.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Oholibama, mkazi wa Esau, mwana wa Ana ndi mdzukulu wa Zebeoni ndi awa: Yeusi, Yolamu ndi Kora.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibeoni, mkazi wace wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Jeusi, ndi Jalamu, ndi Kora.