Genesis 36:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gatamu ndi Amaleke. Ameneŵa ndi mafumu mwa ana a Elifazi m'dziko la Edomu. Onseŵa anali ana a Ada.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mfumu Kora, mfumu Gatamu, mfumu Amaleke: amenewa ndi mafumu a kwa Elifazi m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana amuna a Ada.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kora, Gatamu, ndi Amaleki. Awa anali mafumu mwa ana a Elifazi ku Edomu ndipo onsewa anali zidzukulu za Ada.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mfumu Kora, mfumu Gatamu, mfumu Amaleki: amenewa ndi mafumu a kwa Elifazi m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana amuna a Ada.