Genesis 36:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa ana a Reuele, mwana wa Esau, panali mafumu aŵa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Ameneŵa ndiwo mafumu mwa ana a Ruwele m'dziko la Edomu, ndiponso ndiwo ana a Basemati mkazi wa Esau.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amenewa ndi ana amuna a Reuwele mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reuwele m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana aamuna a Basemati mkazi wake wa Esau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa ana a Reueli, mwana wa Esau munali mafumu awa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. Awa anali mafumu mwa ana a Reueli ku Edomu. Iwowa anali zidzukulu za Basemati mkazi wa Esau.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amenewa ndi ana amuna a Reueli mwana wamwamuna wa Esau: mfumu Nahati, mfumu Zera, mfumu Sama, mfumu Miza; amenewa ndi mafumu obadwa kwa Reueli m'dziko la Edomu: amenewa ndi ana amuna a Basemati mkazi wace wa Esau.