Genesis 36:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Esau adaakwatira akazi Achikanani aŵa: Ada mwana wa Eloni Muhiti, Oholibama mwana wa Ana, mwana wa Zibiyoni Muhivi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Esau anatenga akazi ake a ana akazi a m'Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Muhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni Muhivi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Esau anakwatira akazi atatu a ku Kanaani. Iwowa ndiwo Ada mwana wa Eloni Mhiti; Oholibama mwana wa Ana amene anali mwana wa Zibeoni Mhivi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Esau anatenga akazi ace a ana akazi a m'Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Mhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibeoni Mhivi;