Genesis 36:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Lotani anali Hori ndi Hemani, ndipo Timna anali mlongo wa Lotani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Lotani anali Hori ndi Hemani: mlongo wake wa Lotani anali Timna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Lotani anali awa: Hori ndi Homamu. Timna anali mlongo wake wa Lotani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Lotani anali Hori ndi Hemamu: mlongo wace wa Lotani anali Timna.