Genesis 36:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Sobali ndi aŵa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Sobala ndi awa: Alivani ndi Manahati ndi Ebala, Sefo ndi Onamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Sobala anali awa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Sobali ndi awa: Alivani ndi Manahati ndi Ebali, Sefo ndi Onamu.