Genesis 36:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana aamuna a Disoni ndi aŵa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Disoni ndi awa: Hemudani ndi Esibani ndi Itirani, ndi Kerani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Disoni anali awa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Disoni ndi awa: Hemadani ndi Esibani ndi Itirani, ndi Kerana.