Genesis 36:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Ezere ndi aŵa: Bilihani, Zaavani ndi Akani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Ezere ndi awa: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Akani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Ezeri anali awa: Bilihani, Zaavani ndi Akani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Ezeri ndi awa: Biliha, ndi Zavani, ndi Akani.