Genesis 36:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi Basemati mwana wa Ismaele, mlongo wa Nebayoti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Basemati mwana wamkazi wa Ismaele, mlongo wake wa Nebayoti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi Basemati mwana wa Ismaeli, amenenso anali mlongo wa Nabayoti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Basemati mwana wamkazi wa lsmayeli, mlongo wace wa Nabayoti.