Genesis 36:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bela mwana wa Beori, ankalamulira dziko la Edomu, ndipo dzina la mzinda wake linali Dinihaba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Bela mwana wamwamuna wa Beori, analamulira m'Edomu, ndipo dzina la mudzi wake ndilo Dinihaba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bela mwana wa Beori anakhala mfumu ya ku Edomu. Mzinda wake ankawutcha Dinihaba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Bela mwana wamwamuna wa Beori, analamulira m'Edomu, ndipo dzina la mudzi wace ndilo Dinaba.