Genesis 36:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yobabu atafa, Husamu wa ku dziko la Atemani adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yobabu anamwalira, ndipo Husamu wa ku dziko la Atemani analamulira m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atafa Yobabu, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa mʼmalo mwake ngati mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jobabi anamwalira, ndipo Husami wa ku dziko la Atemani analamulira m'malo mwaceo