Genesis 36:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atafa Samila, Shaulo wa ku Rehoboti, mzinda wa pa mtsinje wa Yufurate, ndiye amene adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samila anamwalira, ndipo Shaulo wa ku Rehoboti pambali pa nyanja analamulira m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje, analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Samila anamwalira, ndipo Sauli wa ku Rehoboti pambali pa Nyanja analamulira m'malo mwaceo