Genesis 36:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aŵa ndiwo mafumu a kubanja kwa Esau mwatsatanetsatane, malinga ndi mafuko ao ndi malo a fuko lililonse: Timna, Aliva, Yeteti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maina a mafumu obadwa kwa Esau, monga mabanja ao, monga malo ao, monga maina ao ndi awa: mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Yeteti:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayina a mafumu ochokera mwa zidzukulu za Esau malingana ndi mafuko awo ndi malo a fuko lililonse anali awa: Timna, Aliva, Yeteti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maina a mafumu obadwa kwa Esau, monga mabanja ao, monga malo ao, monga maina ao ndi awa: mfumu Timna, mfumu Aliva, mfumu Jeteti: