Genesis 36:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magadiele ndi Iramu. Ameneŵa ndiwo mafumu a Edomu (ndiye kuti Esau kholo la Aedomu potsatana ndi malo omwe ankakhala m'dziko laolo.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mfumu Magadiele, mfumu Iramu; amenewa ndi mafumu a Edomu, monga mwa kukhala kwao m'dziko lokhala laolao. Uyo ndiye Esau atate wao wa Aedomu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu molingana ndi malo awo okhala mʼdzikomo. Umenewu ndi mndandanda wa mʼbado wa Esau, kholo la Aedomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mfumu Magidieli, mfumu Iramu; amenewa ndi mafumu a Edomu, monga mwa kukhala kwao m'dziko lokhala laolao. Uyo ndiye Esau atate wao wa Aedomu.