Genesis 37:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthuyo adati, “Adachoka kale kuno. Ndidaŵamva akunena kuti akupita ku Dotani.” Apo Yosefe adaŵalondola abale akewo, nakaŵapeza ku Dotani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthuyo ndipo anati, Anachoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotani. Yosefe ndipo anatsata abale ake, nawapeza ali ku Dotani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo anayankha nati, “Anasamukako kuno. Ndinawamva akuti, ‘Tiyeni tipite ku Dotani.’ ” Choncho Yosefe analondola abale ake ndipo anakawapeza ku Dotani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthuyo ndipo anati, Anacoka pano; pakuti ndinamva alinkuti, Timuke ku Dotana. Yosefe ndipo anatsata abale ace, nawapeza ali ku Dotana.