Genesis 37:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo ankauzana kuti, “Uyotu kamaloto uja, akudza apoyo!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati wina ndi mnzake, Taonani, alinkudza mwini maloto uja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anawuzana nati, “Uyo akubwera apo wamaloto uja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati wina ndi mnzace, Taonani, alinkudza mwini maloto uja.