Genesis 37:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tingomuponya m'chitsime chopanda madzichi kuchipululu konkuno. Tisampweteke konse.” Ankanena zimenezi akuganiza zomupulumutsa m'manja mwao, kuti amtumize kwa bambo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'chipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye m'manja mwao, ambwezenso kwa atate wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tisakhetse magazi. Tiyeni timuponye mʼchitsime ku chipululu konkuno. Koma tisamuvulaze nʼkomwe. Rubeni ananena zonsezi kuti apulumutse Yosefe ndi kuti pambuyo pake akamupereke kwa abambo awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'cipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye ra'manja mwao, ambwezenso kwa atate wace.