Genesis 37:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adabwerera kwa abale ake aja naŵauza kuti, “Mnyamata ujatu palibe! Tsono ine ndichite chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anabwera kwa abale ake, nati, Mwana palibe; ndipo ine ndipita kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nabwerera kwa abale ake nati, “Mnyamata uja mulibemo! Nanga ndilowere kuti ine tsopano?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anabwera kwa abale ace, nati, Mwana palibe; ndipo ine ndipita kuti?