Genesis 37:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo iwo adapha mbuzi, naviika mkanjo wa Yosefe uja m'magazi ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga malaya ake a Yosefe, napha tonde, naviika malaya m'mwazi wake:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anapha kamwana ka mbuzi, natenga mkanjo wa Yosefe ndi kuwunyika mʼmagazi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga malaya ace a Yosefe, napha tonde, nabvika malaya m'mwazi wace: