Genesis 37:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adauzindikira mkanjowo, nati, “Ha, ndi wakedi! Chilombo chamupha mwana wanga. Kalanga ine, Yosefe wakadzulidwa!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anazindikira nati, Ndiwo malaya a mwana wanga: wajiwa ndi chilombo: Yosefe wakadzulidwa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawuzindikira ndipo anati, “Ndi mkanjo wa mwana wanga umenewu! Nyama yakuthengo yolusa yamudya. Mosakayika, mwana wanga Yosefe wakhadzulidwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anazindikira nati, Ndiwo malaya a mwana wanga: wajiwa ndi cirombo: Yosefe wakadzulidwa ndithu.