Genesis 37:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adang'amba zovala zake, navala chiguduli m'chiwuno, chifukwa cha chisoni. Adalira maliro a mwana wakeyo nthaŵi yaitali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yakobo ndipo anang'amba malaya ake, navala chiguduli m'chuuno mwake namlirira mwana wake masiku ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yakobo anangʼamba zovala zake, navala chisaka mʼchiwuno mwake. Iye analira maliro a mwana wake masiku ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yakobo ndipo anang'amba malaya ace, nabvala ciguduli m'cuuno mwace namlirira mwana wace masiku ambiri.