Genesis 37:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo nkuti Amidiyani aja atamgulitsa Yosefe kwa Potifara ku Ejipito. Potifarayo anali mmodzi mwa nduna za Farao, ndipo anali mkulu wa asilikali olonda kunyumba kwa Farao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amidiyani ndipo anamgulitsa iye anke ku Ejipito kwa Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amidiyani aja anagulitsa Yosefe kwa Potifara, mmodzi mwa nduna za Farao ku Igupto. Potifarayu anali mkulu wa asilikali olonda nyumba ya Farao.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amidyani ndipo anamgulitsa iye anke ku Aigupto kwa Potifara, nduna ya Farao, kazembe wa alonda.