Genesis 38:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wina adauza Tamara kuti, “Apongozi ako akupita ku Timna kukameta nkhosa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamara atamva kuti apongozi ake akupita ku Timna kukameta nkhosa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamuuza Tamara, kuti, Taona, mpongozi wako akwera kunka ku Timna kuti akasenge nkhosa zace.