Genesis 38:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Itakwana nthaŵi yakuti Tamara achire, m'mimba mwake munali mapasa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali nthawi ya kubala kwake, taonani, amapasa anali m'mimba mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Tamara nthawi inamukwanira yoti abeleke, mʼmimbamo munali mapasa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali nthawi ya kubala kwace, taonani, amapasa anali m'mimba mwace.