Genesis 38:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkaziyo adatenga pathupi nabala mwana wamwamuna, nkumutcha Ere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Eri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatenga pathupi, nabala mwana wamwamuna amene anamutcha Eri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Eri.