Genesis 38:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatenganso pena pathupi nabala mwana wamwamuna, nkumutcha Onani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna, namutcha dzina lake Onani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatenganso pathupi nabala mwana wa mwamuna ndipo anamutcha Onani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna, namucha dzina lace Onani.