Genesis 38:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yuda adampezera mkazi mwana wake wachisamba uja Ere, dzina lake Tamara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yuda anamtengera Eri mwana wake woyamba mkazi, ndipo dzina lake ndilo Tamara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yuda anamupezera mkazi mwana wake woyamba uja Eri, ndipo dzina la mkaziyo linali Tamara.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yuda anamtengera Eri mwana wace woyamba mkazi, ndipo dzina lace ndilo Tamara.