Genesis 38:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yuda adauza Onani kuti, “Loŵana naye mkazi wamasiye wa mbale wakoyu. Uloŵe chokolo ndithu, kuti mbale wakoyo akhale ndi ana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yuda anati kwa Onani, Lowani naye mkazi wa mbale wako, ndi kumchitira mkazi zoyenera mphwake wa mwamuna wake, ndi kumuukitsira mkulu wako mbeu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yuda anati kwa Onani, “Kwatira mkazi wamasiye wa mʼbale wako. Ulowe chokolo kuti mʼbale wako akhale ndi mwana.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yuda anati kwa Onani, Lowani naye mkazi wa mbale wako, ndi kumcitira mkazi zoyenera mphwace wa mwamuna wace, ndi kumuukitsira mkuru wako mbeu.