Genesis 39:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsiku lina Yosefe adaloŵa m'nyumba kuti agwire ntchito, ndipo panalibe antchito ena m'nyumbamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali, nthawi yomweyo, iye analowa m'nyumba kuti agwire ntchito yake; ndipo munalibe amuna a m'nyumba m'katimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina Yosefe analowa mʼnyumbamo kukagwira ntchito zake, ndipo munalibe wina aliyense wantchito mʼnyumbamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali, nthawi yomweyo, iye analowa m'nyumba kuti agwire nchito yace; ndipo munalibe amuna a m'nyumba m'katimo.