Genesis 39:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkazi uja ataona kuti Yosefe wasiya mwinjiro ndipo wathaŵira pabwalo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene mkazi anaona kuti anasiya chofunda chake m'dzanja lake, nathawira kubwalo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mkazi uja anaona kuti Yosefe wamusiyira mkanjo wake mʼmanja mwake nathawira kunja kwa nyumba,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene mkazi anaona kuti anasiya copfunda cace m'dzanja lace, nathawira kubwalo,