Genesis 39:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atamva kukuwa kwangako, wasiya mwinjiro wake m'manja mwangamu nkuthaŵira pabwalo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chofunda chake kwa ine nathawira kubwalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atandimva ndikukuwa, anandisiyira mkanjo wakewu nʼkuthawira kunja.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo panali pamene iye anamva kuti ndinakweza mau anga ndi kupfuula, iye anasiya copfunda cace kwa me nathawira kubwalo.