Genesis 39:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atabwera, adamsimbira nkhani yonseyo, adati, “Kapolo uja Wachihebri mudabwera naye m'nyumba munoyu, analoŵa kuchipinda kwanga kukandipunza ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena kwa iye monga mau awa, anati, Analowa kwa ine kapolo wa Chihebri uja, munabwera naye kwathu, kundipunza ine:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anamuwuza nkhaniyi nati: “Wantchito Wachihebri amene munatibweretsera uja anabwera kuti adzagone nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena kwa iye monga mau awa, nati, Analowa kwa ine kapolo wa Cihebri uja, munabwera naye kwathu, kundipunza ine: