Genesis 39:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine nditakuwa, iyeyo anasiya mwinjiro wake pafupi ndi ine, nkuthaŵira pabwalo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo panali pamene ndinakweza mau anga ndi kufuula, iye anasiya chovala chake kwa ine, nathawira kunja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene ndinakuwa, iye anandisiyira mkanjo wake nathawira kunja.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo panali pamene ndinakweza mau anga ndi kupfuula, iye anasiya cobvala cace kwa ine, nathawira kunja.