Genesis 40:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita kanthaŵi, munthu woperekera vinyo pamodzi ndi wopanga buledi ku nyumba ya mfumu ya ku Ejipito, adalakwira mbuyao mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali zitapita izi, wopereka chikho wa mfumu ya Aejipito ndi wophika mkate wake anamchimwira mbuye wao mfumu ya Aejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi, woperekera zakumwa ndi wopanga buledi a ku nyumba kwa mfumu ya ku Igupto analakwira mbuye wawoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali zitapita izi, wopereka cikho wa mfumu ya Aigupto ndi wophika mkate wace anamcimwira mbuye wao mfumu ya Aigupto.