Genesis 40:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakangopita masiku atatu, Farao akutulutsa muno, akukhululukira, ndipo akubwezera pa ntchito yako. Tsono uzidzaperekera chikho kwa Farao monga momwe unkachitira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akali masiku atatu Farao adzatukula mutu wako, nadzabwezera iwe ntchito yako; ndipo udzapereka chikho cha Farao m'dzanja lake, monga kale lomwe m'mene unali wopereka chikho chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakangopita masiku atatu, Farao adzakutulutsa muno. Udzaperekera zakumwa kwa Farao monga momwe umachitira poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akali masiku atatu Farao adzatukula mutu wako, nadzabwezera iwe nchito yako; ndipo udzapereka cikho ca Farao m'dzanja lace, monga kale lomwe m'mene unali wopereka cikho cace.