Genesis 40:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komatu udzandikumbuke, zinthu zikadzakuyendera bwino. Chonde udzandikomere mtima ndi kutchula dzina langa kwa Farao, kuti ndidzatulule m'ndende muno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma undikumbukire ine m'mene kudzakhala bwino ndi iwe, ndipo undichitiretu ine kukoma mtima: nunditchule ine kwa Farao, nunditulutse ine m'nyumbamu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zako zikakuyendera bwino, udzandikumbukire ndi kundikomera mtima. Chonde ukandipepesere kwa Farao kuti anditulutse muno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma undikumbukire ine m'mene kudzakhala bwino ndi iwe, ndipoundicitiretu ine kukoma mtima: nundichule ine kwa Farao, nunditurutse ine m'nyumbamu: