Genesis 40:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'nsengwa yapamwamba munali mitundu yambiri ya chakudya cha Farao, koma mbalame zinalikudya chakudyacho.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
m'lichero lapamwamba munali mikate ya Farao ya mitundumitundu; ndipo mbalame zinadya ya m'lichero la pamutu panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mu nsengwa yapamwamba munali zakudya zamitundumitundu za Farao, koma mbalame zimadya zakudyazo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
m'licelo lapamwamba munali mikate ya Farao ya mitundu mitundu; ndipo mbalame zinadya ya m'licelo la pamutu panga.