Genesis 40:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosefe adamuyankha kuti, “Kamasulidwe kake ka maloto ameneŵa ndi aka: nsengwa zitatu ndi masiku atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe anayankha nati, Kumasulira kwake ndi uku: malichero atatu ndiwo masiku atatu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosefe anati, “Tanthauzo lake ndi ili: nsengwa zitatuzo ndi masiku atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe anayankha nati, Mmasuliro wace ndi uwu: malicelo atatu ndiwo masiku atatu;