Genesis 40:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa muno, ndipo adzadula mutu wako. Tsono mtembo wako adzaupachika pa mtengo, ndipo mbalame zidzadya mnofu wako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akali masiku atatu Farao adzakweza mutu wako ndi kuuchotsa, nadzakupachika iwe pamtengo: ndipo mbalame zidzadya mnofu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakangotha masiku atatu Farao adzakutulutsa muno koma adzakupachika. Ndipo mbalame zidzadya mnofu wako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akali masiku atatu Farao adzakweza mutu wako ndi kuucotsa, nadzakupacika iwe pamtengo: ndipo mbalame zidzadya mnofu wako.