Genesis 40:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma wophika buledi uja adampachika, monga momwe Yosefe adaanenera pomasulira maloto ao aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anampachika wophika mkate wamkulu; monga Yosefe anawamasulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma mkulu wa ophika buledi anamupachika, mofanana ndi mmene Yosefe anatanthauzira maloto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anampacika wophika mkate wamkuru; monga Yosefe anawamasulira.