Genesis 40:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkulu wa alonda uja adasankhula Yosefe kuti asamalire anthu aŵiriwo ndi kuŵalonda. Adakhalamo nthaŵi yaitali ndithu m'ndendemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kazembe wa alonda anapereka iwo kwa Yosefe, ndipo iye anawatumikira iwo: ndipo anakhala nthawi mosungidwamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkulu wa alonda aja anawapereka mʼmanja mwa Yosefe, ndipo iye anawasamalira. Iwo anakhala mʼndendemo kwa kanthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kazembe wa alonda anapereka iwo kwa Yosefe, ndipo iye anawatumikira iwo: ndipo anakhala nthawi mosungidwamo.