Genesis 40:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosefe atabwera m'maŵa, adaona kuti nkhope zao zasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe analowa kwa iwo m'mawa, nawaona iwo, taonani, anali oziya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa wake, Yosefe atabwera, anaona kuti nkhope zawo zinali zakugwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe analowa kwa iwo m'mawa, nawaona iwo, taonani, anali oziya.