Genesis 40:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵafunsa kuti, “Mwatani mukuwoneka ngati achisoni lero?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anafunsa akulu a Farao osungidwa naye m'nyumba ya mbuyake, kuti, Nkhope zanu zagwa bwanji lero?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anafunsa akuluakulu a kwa Farao amene anali naye mʼndende muja kuti, “Bwanji nkhope zanu zili zachisoni lero?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anafunsa akuru a Farao osungidwa naye m'nyumba ya mbuyace, kuti, Nkhope zanu zagwa bwanji lero?