Genesis 41:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja inu mfumu mudaatipsera mtima antchitofe. Ndipo ine ndi wophika buledi tonse mudaatitsekera m'ndende, m'nyumba ya mkulu wa alonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Farao anakwiya ndi anyamata ake, nandiika ine ndisungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, ine ndi wophika mkate wamkulu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Paja nthawi ina Farao anapsera mtima antchito akefe, ndipo anatitsekera (ine ndi mkulu wa ophika buledi) mʼndende, mʼnyumba ya mkulu wa alonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Farao anakwiya ndi anyamata ace, nandiika ine ndisungidwe m'nyumba ya kazembe wa alonda, ine ndi wophika mkate wamkuru: