Genesis 41:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Farao adauza Yosefe kuti, “Ine ndidalota maloto, koma palibe ndi mmodzi yemwe amene akutha kumasula malotowo. Tsono adandiwuza kuti iwe ukamva maloto, ati umadziŵa kumasula kwake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Farao ndipo anati kwa Yosefe, Ine ndalota loto, koma palibe wondimasulira; ndipo ndamva alikunena za iwe kuti, ukamva loto udziwa kumasulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao anati kwa Yosefe, “Ndinalota maloto ndipo palibe amene watha kunditanthauzira. Tsono ndawuzidwa kuti iwe ukamva loto umadziwanso kulimasulira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Farao ndipo anati kwa Yosefe, Ine ndalota loto, koma palibe wondimasulira; ndipo ndamva alikunena za iwe kuti, ukamva loto udziwa kumasulira.