Genesis 41:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yomweyo ndidangoona ng'ombe zisanu ndi ziŵiri zonenepa bwino zitatuluka mumtsinjemo, nkuyamba kudya msipu wam'mabango.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo taona, zinatuluka m'nyanjamo ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri, zonenepa ndi za maonekedwe abwino; ndipo zinadya m'mabango;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ngʼombe zisanu ndi ziwiri zonenepa ndi zooneka bwino zinatuluka mu mtsinje muja ndi kumadya msipu wa mu mawango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo taona, zinaturuka m'nyanjamo ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri, zonenepa ndi za maonekedwe abwino; ndipo zinadya m'mabango;