Genesis 41:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nditagonanso ndidalota ntaona ngala zatirigu zisanu ndi ziŵiri zakucha ndi zokhwima bwino zitabala pa mphesi imodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinauka. Ndipo ndinaona m'kulota kwanga, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zinamera pa mbuwa imodzi zodzala ndi zabwino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nditagonanso kachiwiri, ndinalota ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zathanzi ndi zonenepa zitabala pa phata limodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinauka. Ndipo ndinaona m'kulota kwanga, taona, ngala zisanu ndi ziwiri zinamera pa mbuwa imodzi zodzala ndi zabwino;