Genesis 41:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono monga momwe ndanenera, ndiye kuti Mulungu wakuuziranitu zomwe adzachite.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi chinthu chimene ndinena kwa Farao: chimene Mulungu ati achite wasonyeza kwa Farao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono ndi monga ndafotokozeramu kuti Mulungu wakuwuziranitu zimene adzachite.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi cinthu cimene ndinena kwa Farao: cimene Mulungu ati acite wasonyeza kwa Farao.