Genesis 41:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zaka zonse zija za dzinthu dzambiri sizidzakumbukikanso, chifukwa njala imene idzabwereyo idzakhala yoopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo zochuluka sizidzazindikirika chifukwa cha njala ikudza m'mbuyoyo, pakuti idzavuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zakudya zochuluka za mʼdzikomo zija sizidzakumbukirikanso chifukwa njala imene iti idzabwereyo idzakhala yoopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo zocuruka sizidzazindikirika cifukwa ca njala ikudza m'mbuyoyo, pakuti idzabvuta.